Genesis Chaputala 1 (CCL) — Chilengedwe & Spoken Audio
Poyamba Mulungu analenga thambo ndi dziko lapansi. Dziko linali losaumbika ndiponso lopanda kanthu, ndipo mdima unali pachozama, ndipo Mzimu wa Mulungu unkayendayenda pa madzi.
Scripture Text Preview — Genesis Chaputala 1 (CCL) — Chilengedwe & Spoken Audio
1. Poyamba Mulungu analenga thambo ndi dziko lapansi.
2. Dziko linali losaumbika ndiponso lopanda kanthu, ndipo mdima unali pachozama, ndipo Mzimu wa Mulungu unkayendayenda pa madzi.
3. Mulungu anati, “Kukhale kuwala,” ndipo kunakhala kuwala.
4. Mulungu anaona kuti kuwalako kunali kwabwino, ndipo anasiyanitsa kuwala ndi mdima.
5. Mulungu anatcha kuwalako “Usana,” ndipo mdimawo anawutcha “Usiku.” Ndipo panali madzulo, kenaka m’mawa: tsiku loyamba.
Parallel Bible Study, Strong’s Concordance, 24kHz Audio & Offline Vault
Compare this passage side-by-side in up to 4 synchronized columns across NKJV, KJV, BSB, Original Hebrew (WLC), Koine Greek (Textus Receptus), Asante Twi (Twerɛ Kronkron), French, Spanish, German, and 35+ global languages on AduBible.org®. Tap any verse for Strong’s Exhaustive Concordance numbers, Matthew Henry & John Gill commentaries, 24kHz Neural Audio streaming, and 100% offline PWA access.